No. ENGLISH PHRASE CHICHEWA PHRASE
1 Welcome Takulandirani
2 How are you? Muli bwanji?
3 I am fine Ndili bwino
4 Thank you Zikomo
5 Thank you so much Zikomo kwambiri
6 What is your name? Dzina lanu ndani?
7 My name is Dzina langa ndi...
8 I am tired Ndatopa
9 I am very tired Ndatopa
10 Sorry Pepani
12 It is hot/ It is sunny Kukutentha/Kuli dzuwa
13 It is very hot Kukutentha Kwambiri
14 Where are you? Muli kuti?
15 Please Chonde
16 Come please Tabwera chonde
17 Come fast please Tabwerani mwachangu chonde
18 Enter Lowani
19 Help me Ndithandizeni
20 Slowly please Pang'onopang'ono chonde
21 Stop! Imani!
22 We have arrived! Tafika!
23 Am happy Ndakondwera
24 Water Madzi
25 I need water Ndikufuna madzi
26 Food Chakudya
27 I need food Ndikufuna Chakudya
28 I am hungry Ndili ndi njala
29 Is there food? Pali chakudya?
30 Do you know? Makudziwa?
31 I don't know Sindikudziwa
32 A little Pang'ono
33 Yes Eya
34 No Ayi
35 Nice food Chakudya chabwino
36 I am happy Ndili okondwa
37 Money Ndalama
38 How much money? Ndilibe ndalama
39 I don't have money Ndilibe ndalama
40 I want to rest Ndikufuna ndipume
41 Go away Chokani
42 Good night Usiku wabwino
43 See you/Goodbye Tionana
44 I love you Ndimakukondani
45 Family Banja
46 Your family Banja lanu
47 I miss you Ndakusowani
48 Good morning Mwadzuka bwanji
49 Let us go! Tiyeni!
50 You/You Iwe/Inu (Singular/Plural)
51 Your family Banja Lanu
52 Father/Man Bambo
53 Mother/Woman Mayi
54 Children Ana
55 Your Wako/Ako (Singular/Plural)
56 Husband Mamuna
57 Wife Mamuna
58 Road Nseu
59 Good road Nseu wabwino
60 Bad road Nseu oipa
61 Safe Trip/Travel well Muyende bwino
62 We shall possibly meet again Mwina tizaonananso